LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp17 na. 5 masa. 1-2
  • Angelo Kodi Aliko Zoona? Cifukwa Cake Tifuna Kudziŵa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Angelo Kodi Aliko Zoona? Cifukwa Cake Tifuna Kudziŵa
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
wp17 na. 5 masa. 1-2
Nsanja ya Mlonda Na. 5, 2017 | Angelo​—Kodi Aliko Zoona? Cifukwa Cake Tifuna Kudziŵa

Angelo Kodi Aliko Zoona? Cifukwa Cake Tifuna Kudziŵa

Na. 5 2017

© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.

Kuti mucite copeleka, yendani pa webusaiti ya www.jw.org.

Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ni Wolamulila wa cilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti posacedwa, Ufumu wa Mulungu udzacotsa zoipa zonse na kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsa anthu kukhulupilila Yesu Khristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha, ndipo panthawi ino iye akulamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magaziniyi yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879 ndipo si yandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani