Mau Oyamba
MUGANIZA BWANJI?
Kodi angelo aliko zoona? Baibo imati:
“Tamandani Yehova, inu angelo ake amphamvu, ocita zimene wanena, mwa kumvela malamulo ake.”—Salimo 103:20.
Nsanja ya Mlonda iyi ionetsa zimene Baibo imakamba ponena za angelo, na mmene amakhudzila umoyo wathu.