Zamkati
WIKI YA JULY 31, 2017–AUGUST 6, 2017
4 Yehova Amatitonthoza m’Masautso Athu Onse
Tonse timakumana ndi mavuto. Koma Yehova amatitonthoza. Nkhani iyi idzafotokoza zinthu zofunika zimene zingatithandize kupeza citonthozo panthawi ino ndi mtsogolo.
WIKI YA AUGUST 7-13, 2017
9 Ikani Mtima Wanu pa Cuma Cauzimu
Nkhani iyi, idzatithandiza kudziŵa mmene tingaseŵenzetsela mfundo ya m’fanizo la Yesu la wamalonda amene anali kusakila ngale. Idzatithandizanso kudzipenda ndi kuona mmene ise patekha, timaonela utumiki wopulumutsa moyo umene Akhristufe tinapatsidwa, ndi coonadi cimene takhala tikuphunzila zaka zonsezi.
14 Musamaone Cabe Maonekedwe a Munthu
16 Kodi Mudzakambilana Kuti Muthetse Mkangano ndi Kulimbikitsa Mtendele?
21 “Udalitsike Cifukwa ca Kulingalila Bwino Kwako”
WIKI YA AUGUST 14-20, 2017
22 Muziika Maganizo Anu pa Nkhani Yaikulu
WIKI YA AUGUST 21-27, 2017
27 Muzicilikiza Ulamulilo wa Yehova
Cifukwa cotangwanika na zocitika pa umoyo, cingakhale cosavuta kuiŵala zinthu zofunika. Nkhani izi zidzatithandiza kumvetsa kufunika kwa ulamulilo wa Yehova ndi kudziŵa mmene tingaucilikizile.