Yophunzila
SEPTEMBER 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: OCTOBER 29–DECEMBER 2, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
IRELAND
Abale na alongo ali pa ulendo wopita ku zisumbu za Aran Islands, zimene zili kumadzulo kwa dziko la Ireland. Akupita kukalalikila uthenga wabwino kwa anthu a kumeneko, m’citundu ca Ciairishi
OFALITSA
6,747
MAPHUNZILO A BAIBO
3,392
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
12,082
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mupeleke copeleka canu, yendani pa webusaiti ya www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.