Kodi Mulungu N’ndani?
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Ngati mufuna kupeleka zothandizila pa nchitoyi, yendani pa www.jw.org. Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.
MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ni Wolamulila wa cilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu na uthenga wabwino wakuti posacedwa Ufumu wa Mulungu udzacotsapo zoipa zonse, na kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsanso anthu kukhulupilila Yesu Khristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha. Ndipo panthawi ino, iye alamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magazini ino yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879, ndipo siiloŵelela m’nkhani zandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibo.