Yophunzila
JANUARY 2019
NKHANI ZOPHUNZILA: MARCH 4–APRIL 7, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Ngati mufuna kupeleka zothandizila pa nchitoyi, yendani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO:
Anthu mamiliyoni ambili pa dziko lonse lapansi adzalandilidwa pa Mgonelo wa Ambuye (Onani nkhani yophunzila 5, palagilafu 1-2)