Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
TSANZILANI CIKHULUPILILO CAWO
Eliya—Anapilila Mpaka Pamapeto
Citsanzo ca Eliya ca kupilila mokhulupilika cingalimbitse cikhulupililo cathu pamene tikumana na mavuto.
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUKHULUPILILA MULUNGU.)
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Munthu wina amene kale anali m’gulu la zigaŵenga anasintha, ndipo amaona kuti kusintha kwake ni umboni wakuti Baibo ili na mphamvu yosintha anthu. Tsopano iye ali pa ubale wolimba na Mulungu.
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDELE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)