Zina Zimene Zilipo pa JW.ORG
KODI ZINANGOCITIKA ZOKHA?
Kaulukidwe Kodabwitsa ka Nchenche
Nchenche zimatha kutembenuka ngati ndeke zankhondo, koma zimacita zimenezi m’kanthawi kocepa, kosakwana ngakhale sekondi imodzi. Kodi n’ndani anapatsa nchenche luso louluka?
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI.)
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Zinkaoneka Ngati Zinthu Zikundiyendera
Pamene Stéphane anali wacinyamata anali wochuka komanso wa cuma, koma anali kudzimva kukhala wopanda pake ndiponso wosakhutila na umoyo wake. Kodi anapeza bwanji cimwemwe ceni-ceni komanso colinga ca moyo?
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDELE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)