Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Mphotho Yaikulu Kwambili pa Moyo Wanga
N’ciani cinasonkhezela katswili wina wamaseŵela a tenesi kuleka nchitoyi, imene anali kuikonda kwambili n’kuyamba utumiki wanthawi zonse?
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDERE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Mumakonda Mwamuna Kapena Mkazi Wanu?
Kodi anthu okwatilana angaonetse bwanji kuti amakondanadi? Pali mfundo zinayi za m’Baibo zimene zingakuthandizeni pa nkhaniyi.
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA.)