Zina Zimene Zilipo Pa Jw Laibulale Na Pa Jw.Org
KODI ZINANGOCITIKA ZOKHA?
Luso la Dolphin Lozindikila Zinthu Mosavuta
Asayansi akuyesetsa kutengela luso la Dolphin lozindikila zinthu mosavuta, pofuna kupanga zipangizo zimene zingawathandize kudziŵa zimene zikucitika m’madzi.
Pa JW Laibulale, ku Chichewa, pitani pa PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > WAS IT DESIGNED?
Pa jw.org, ku Chichewa, pitani pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Mungathandize Bwanji Mwana Wanu Kuti Azikhoza Bwino Kusukulu?
Mwana wanu akamapanikizika, amayamba kukhala ndi nkhawa akakhala kusukulu ndiponso kunyumba. Makolo angadziŵe vuto limene likucititsa mwana wawo kuti asamakhoze bwino komanso mmene angamuthandizile.