Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Ndingatani Kuti Ndizigawa Bwino Nthawi Yanga?
Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti muzipewa kuwononga nthawi yanu.
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAM ATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Guluu wa Kanyama Kochedwa Barnacle
Guluu wa kanyama kameneka amamata mwamphamvu kwambili kuposa guluu aliyense wopangidwa ndi anthu. Posacedwapa, asayansi atulukila zimene zimathandiza kuti kanyamaka kazimamatila kwambili pamalo pamene pali madzi.
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?