Zilengezo
◼ Zogaŵila mu: January ndi February: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu kapena kamodzi mwa tumabuku twa masamba 32 totsatila: Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kapena kakuti Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu!, Mvetsalani kwa Mulungu, ndi kakuti Mvetselani Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. March ndi April: Gaŵilani magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani!
◼ Kuyambila ndi Nsanja ya Mlonda ya July 15, 2014, tizikhala ndi Nsanja ya Mlonda yophunzila m’Cinyanja. Ndipo tizikhalanso ndi yogaŵila imene izituluka pakapita miyezi iŵili kuyambila ndi ya July-August 2014.