LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsa. 7
  • Esitere Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Esitere Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Esitere Anaimila Yehova ndi Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Esitere Apulumutsa Anthu a Mtundu Wake
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Mordekai Ndi Estere
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 February tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | ESITERE 1–5

Esitere Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu

Esitere anaonetsa cikhulupililo camphamvu ndiponso kulimba mtima poteteza anthu a Mulungu

  • Aliyense wopita kukaonekela kwa Mfumu osaitanidwa anali kuphedwa. Panali patapita masiku 30 Esitere asanaitanidwe kukaonekela kwa mfumu

  • Mfumu Ahasiwero amene anthu ambili amakhulupilila kuti anali Sasita woyamba, anali ndi mtima wapacala kwambili. Panthawi ina, iye analamula kuti munthu wina adulidwe pakati, ndipo mtembo wake uikidwe poonekela kuti anthu ena atengelepo phunzilo. Ahasiwero anacotsanso Vasiti paufumukazi cifukwa cakuti anakana kumvela zonena zake

  • Esitere anafunika kuulula kuti anali Myuda ndi kuthandiza mfumu kutsimikizila kuti mlangizi wake amene anali kum’khulupilila kwambili anali atam’namiza

Mfumukazi Esitere wagwila pamwamba pa ndodo imene Mfumu Ahasiwero yamulata nayo m’nyumba yacifumu
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani