LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp20 na. 3 masa. 1-2
  • Madalitso Osatha Ocokela kwa Mulungu Wacikondi.

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Madalitso Osatha Ocokela kwa Mulungu Wacikondi.
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
wp20 na. 3 masa. 1-2
Nsanja ya Mlonda, No. 3, 2020 | Madalitso Osatha Ocokela kwa Mulungu Wacikondi.

Madalitso Osatha Ocokela Kwa Mulungu Wacikondi

No. 3 2020

© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza panchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org. Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ni Wolamulila wa cilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu na uthenga wabwino wakuti posacedwa Ufumu wa Mulungu udzacotsapo zoipa zonse, na kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsanso anthu kukhulupilila Yesu Khristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha. Ndipo pa nthawi ino, iye alamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magazini ino yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879, ndipo siiloŵelela m’nkhani zandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani