September 26–October 2
MASALIMO 142–150
Nyimbo 134 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yehova Ndi Wamkulu ndi Woyenela Kutamandidwa Kwambili”: (Mph. 10)
Sal. 145:1-9—Ukulu wa Yehova ndi wosasanthulika (w04 1/15-CN, tsa. 10 ndime 3-4; tsa. 11 ndime 7-8; tsa. 14 ndime 20-21; tsa. 15 tsa. 2)
Sal. 145:10-13—Okhulupilika a Yehova amam’tamanda (w04 1/15-CN, tsa. 16 ndime 3-6)
Sal. 145:14-16—Yehova amacilikiza ndi kusamalila okhulupilika ake (w04 1/15-CN, tsa. 17-18 ndime 10-14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 8)
Sal. 143:8—Kodi vesi imeneyi itithandiza bwanji kulemekeza Mulungu tsiku lililonse? (w10 1/15-CN, tsa. 21 ndime 1-2)
Sal. 150:6—Kodi vesi yothela m’buku la Salimo itilimbikitsa kucita ciani? (it-2 448)
Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 145:1-21
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) 1 Pet. 5:7—Phunzitsani Coonadi.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 37:9-11—Phunzitsani Coonadi.
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) fg phunzilo 9 ndime 3—Thandizani wophunzila kuona mmene angaseŵenzetsele mfundo za m’nkhaniyo.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Limbikitsani Acidwi Kupezeka pa Misonkhano”: (Mph. 15) Kukambilana. Gaŵilani kapepala koitanila anthu ku misonkhano, ndipo kambilanani mwacidule mfundo zili pa tsamba 2. Tambitsani vidiyo yoonetsa ofalitsa akuitanila munthu ku msonkhano pamene agaŵila magazini. Tsilizani mwa kukambilana bokosi yakuti “Cogaŵila mu October: Kapepala Koitanila Anthu ku Misonkhano.”
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) kr mutu 1, ndime 11-20, ndi machati pa tsa. 10, 12
Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 145 na Pemphelo
Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi nyimboyo.