July 3-9
EZEKIELI 11–14
Nyimbo 52 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kodi Muli na Mtima wa Mnofu?”:(10 min.)
Ezek. 11:17, 18—Yehova analonjeza kubwezeletsa kulambila koona (w07 7/1 peji 11 pala. 4)
Ezek. 11:19—Yehova angatipatse mtima wolabadila citsogozo cake (w16.05 peji 17 pala. 9)
Ezek. 11:20—Yehova amafuna kuti tiziseŵenzetsa zimene timaphunzila
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Ezek. 12:26-28—Ni udindo wanji umene mavesiwa apeleka kwa atumiki a Yehova? (w07 7/1 peji 13 pala. 8)
Ezek. 14:13, 14—Tiphunzilapo ciani pakuchulidwa kwa anthu aŵa? (w16.05 peji 30 pala. 13; w07 7/1 peji 13 pala. 9)
Kodi imwe pacanu kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 12:1-10
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (15 min.) Kukambilana “Maulaliki a Citsanzo.” Tambitsani vidiyo imodzi-imodzi, ndipo kambilanani zimene mwaphunzilapo.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.) Apo ayi, kambilanani zimene tiphunzilapo mu Buku Lapacaka. (yb17 peji 41-43)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 14 mapa. 15-23, ndi bokosi lobwelelamo“ Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 43 na Pemphelo