LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 September tsa. 4
  • September 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 September tsa. 4

September 11-17

EZEKIELI 46-48

  • Nyimbo 134 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Madalitso Amene Isiraeli Wobwezeletsedwa Anali Kudzalandila”: (10 min.)

    • Ezek. 47:1, 7-12—Nthaka inali kudzakhalanso yaconde (w99 3/1 peji 10 mapa. 11-12)

    • Ezek. 47:13, 14—Banja lililonse linali kudzalandila coloŵa cake (w99 3/1 peji 10 pala. 10)

    • Ezek. 48:9, 10—Asanagaŵile anthu malo, anali kupatulilatu “gawo” lina kuti likhale “copeleka” kwa Yehova

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Ezek. 47:1, 8; 48:30, 32-34—N’cifukwa ciani Ayuda a ku ukapolo sanayembekezele kuti zonse zokhudza masomphenya a Ezekieli a kacisi adzakwanilitsika mwakuthupi? (w99 3/1 peji 11 pala. 14)

    • Ezek. 47:6—N’cifukwa ciani Ezekieli akuchulidwa kuti “mwana wa munthu”? (it-2 peji 1001)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 48:13-22

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) wp17.5 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) wp17.5—Citani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa magazini imene inagaŵilidwa pa ulendo woyamba. Ndiyeno muonetseni imodzi mwa mabuku athu otsogozela phunzilo la Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. kapena kucepelapo) bhs peji 35 pala. 17—Muitanileni ku misonkhano.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 28

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.) Apo ayi, kambilanani zimene tiphunzilapo mu Buku Lapacaka. (yb17 peji 64-65)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya September.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 17 mapa. 19-20, bokosi “Masukulu Ophunzitsa Atumiki a Ufumu,” na kabokosi kobwelelamo “Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 11 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani