LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 February tsa. 2
  • February 5-11

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 5-11
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 February tsa. 2

February 5-11

MATEYU 12-13

  • Nyimbo 27 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Fanizo la Tiligu ndi Namsongole”: (10 min.)

    • Mat. 13:24-26—Munthu wina anafesa mbewu zabwino m’munda mwake, ndiyeno mdani wake anafesa namsongole m’mundamo (w13 7/1 mape. 15-16 mapa. 2-3)

    • Mat. 13:27-29—Tiligu ndi namsongole zinakulila pamodzi mpaka nthawi yokolola (w13 7/1 peji 16 pala. 4)

    • Mat. 13:30—Pa nthawi yokolola, coyamba okolola anasonkhanitsa namsongole pamodzi, kenako anasonkhanitsa tiligu (w13 7/1 mape. 18-19 mapa. 10-12)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 12:20—Kodi tingatengele bwanji cifundo ca Yesu? (“Nyale Yofuka” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 12:20)

    • Mat. 13:25—Kodi n’zoona kuti kale anthu anali kufesa namsongole m’minda ya anthu ena? (w16.10 peji 32)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 12:1-21

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyo.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 22-23 mapa. 10-12

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 68

  • Zofunikila za Mpingo: (5 min.)

  • “Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise”: (10 min) Kambilanani mmene mafanizo amenewa amakhudzila utumiki wathu.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy Mutu 7

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 10 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani