February 12-18
MATEYU 14-15
Nyimbo 93 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kudyetsa Anthu Ambili Mwa Kugwilitsila Nchito Anthu Ocepa”: (10 min)
Mat. 14:16, 17—Ophunzila anali cabe na mitanda isanu ya mkate na nsomba ziŵili (w13 7/1 peji 21 pala. 2)
Mat. 14:18, 19—Yesu anadyetsa khamu la anthu mwa kuseŵenzetsa ophunzila ake (w13 7/1 peji 21 pala. 3)
Mat. 14:20, 21—Anthu masauzande anapindula na cozizwitsa ca Yesu (“osaŵelengela akazi ndi ana aang’ono” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 14:21; w13 7/1 peji 21 pala. 1)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mat. 15:7-9—N’cifukwa ciani tifunika kupewa kucita zacinyengo? (“onyenga” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 15:7)
Mat. 15:26—Kodi Yesu ayenela kuti anatanthauza ciani pamene anaseŵenzetsa mau akuti “tiagalu”? (“ana . . . tiagalu” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 15:26)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 15:1-20
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w15 9/15 mape. 19-20 mapa. 14-17—Mutu: Kuyang’anitsitsa Yesu Kudzalimbitsa Cikhulupililo Canu.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Khala Bwenzi la Yehova—Kupanga Mabwenzi: (7 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Pambuyo pake, itanani ana amene munasankha kuti abwele ku pulatifomu, na kuwafunsa mafunso aya: N’cifukwa ciani mufunika kupanga ubwenzi na anthu okonda Yehova? Nanga mungaphunzile ciani kwa iwo?
“Uzilemekeza Atate Ako ndi Amayi Ako”: (8 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya tukadoli yakuti Ningakambe Nawo Bwanji Makolo Anga?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 8
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 148 na Pemphelo