LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 March tsa. 3
  • March 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 March tsa. 3

March 12-18

MATEYU 22-23

  • Nyimbo 30 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Muzitsatila Malamulo Aŵili Aakulu a m’Cilamulo”: (10 min.)

    • Mat. 22:36-38—Kodi mavesiwa afotokoza kuti kutsatila Lamulo lalikulu komanso loyamba kumaphatikizapo ciani? (“mtima,” “moyo,” “maganizo” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 22:37)

    • Mat. 22:39—Kodi Lamulo lalikulu laciŵili m’Cilamulo ni liti? (“Laciŵili,” “mnzako” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 22:39)

    • Mat. 22:40—Malemba onse Aciheberi ni ozikidwa pa cikondi (“Cilamulo . . . zolemba za Aneneli,” “cagona” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 22:40)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 22:21—Kodi “zinthu za Kaisara” na zinthu “za Mulungu” n’ciani? (“zinthu za Kaisara kwa Kaisara,” “zinthu . . . za Mulungu kwa Mulungu” nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 23:24—Kodi mau a Yesu amenewa atanthauza ciani?

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 22:1-22

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 199 mapa. 8-9—Mphunzitsi alimbikitse wophunzila kuitanilako ena ku Cikumbutso.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 96

  • “Tingacite Ciani Kuti Tikulitse Cikondi Cathu kwa Mulungu na kwa Mnansi Wathu?”: (15 min.) Kukambilana. Kuti tione kufunika koyelekezela nkhani za m’Baibo m’maganizo mwathu, tiyeni timvetsele seŵelo la m’Baibo la mau cabe lakuti Yehova Ndiye Mulungu Yekha Woona—kambali kake, ndipo gulu litsatile kuŵelengedwa kwa lemba la 1 Mafumu 18:17-46.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 12

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 52 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani