LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 March tsa. 4
  • March 19-25

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 19-25
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 March tsa. 4

March 19-25

MATEYU 24

  • Nyimbo 126 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Khalanibe Ogalamuka m’Masiku Otsiliza Ano”: (10 min.)

    • Mat. 24:12—Kuwonjezeka kwa kusamvela malamulo kudzacititsa cikondi ca anthu kuzilala (it-2 peji 279 pala. 6)

    • Mat. 24:39—Anthu ena adzakhala na nkhawa yaikulu kufuna-funa zinthu zakuthupi, ndipo zidzawacenjeneka (w99 11/15 peji 19 pala. 5)

    • Mat. 24:44—Ambuye adzabwela pa nthawi yosayembekezeleka (jy peji 259 pala. 4)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 24:8—Kodi zimene Yesu anakamba zitipatsa cithunzi canji? (“zoŵaŵa za pobeleka” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 24:8)

    • Mat. 24:20—N’cifukwa ciani Yesu anakamba izi? (“nyengo ya cisanu,” “pa tsiku la sabata” nwtsty mfundo younikila pa Mat. 24:20)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 24:1-22

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Mwininyumba akambe zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Munthu amene munakambilana naye simunamupeze, koma mwapeza m’bululu wake.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 57

  • “Tili ku Mapeto a Dongosolo Lino la Zinthu”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 13

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 97 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani