LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 5
  • Kucilitsa pa Sabata

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kucilitsa pa Sabata
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • “Pali Nthawi” Yogwila Nchito na Nthawi Yopumula
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 5
Munthu wopuwala dzanja afikila Yesu

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 3-4

Kucilitsa pa Sabata

3:1-5

N’cifukwa ciani Yesu anamva cisoni kwambili na zocita za atsogoleli a cipembedzo aciyuda? Cifukwa iwo anapangitsa Sabata kukhala yolemetsa mwa kuwonjezela malamulo ambili ang’ono ang’ono. Mwacitsanzo, kupha nsabwe kapena kuti inda kunali koletsedwa. Anali kulola kucilitsa pokhapo ngati moyo unali paciwopsezo. Izi zinatanthauza kuti munthu akathyoka fupa kapena kuvyungunuka, sanali kufunika kupatsiwa thandizo pa Sabata. Conco, n’zoonekelatu kuti atsogoleli a cipembedzo sanali kumuganizila munthu wopuwala dzanja.

DZIFUNSENI KUTI:

  • ‘Kodi anthu ena amaniona monga munthu wokhwimitsa zinthu kapena wacifundo?

  • ‘Nikaona wina mumpingo amene afunikila thandizo, ningacitenji kuti nitengele cifundo ca Yesu?’

Akulu aŵili apanga ulendo waubusa kwa mlongo wabize na mwana wake wacicepele
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani