LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 September tsa. 2
  • September 3-9

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 3-9
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 September tsa. 2

September 3-9

YOHANE 1-2

  • Nyimbo 13 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yesu Acita Cozizwitsa Cake Coyamba”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Yohane.]

    • Yoh. 2:1-3—Zinacitika pa phwando la cikwati zikanakhala zocititsa manyazi (w15 6/15 peji 4 pala. 3)

    • Yoh. 2:4-11—Cozizwitsa cimene Yesu anacita cinalimbikitsa cikhulupililo ca ophunzila ake (jy peji 41 pala. 6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 1:1—Yohane sanatanthauze kuti wochedwa “Mawu” anali wolingana na Mulungu Wamphamvuzonse. Tikamba conco pa zifukwa ziti? (“Mau,” “anali ndi,” “Mauyo anali mulungu” nwtsty mfundo zounikila)

    • Yoh. 1:29—N’cifukwa ciani Yohane M’batizi anachula Yesu kuti “Mwanawankhosa wa Mulungu”? (“Mwanawankhosa wa Mulungu” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 1:1-18

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 50, Mfundo 2

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 38

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya September.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 mapa. 12-19

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 121 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani