September 24-30
YOHANE 7-8
Nyimbo 12 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yesu Analemekeza Atate Wake”: (10 min.)
Yoh. 7:15-18—Yesu amati akatamandidwa pa kaphunzitsidwe kake, anali kupeleka citamandoco kwa Yehova (cf mape. 100-101 mapa. 5-6)
Yoh. 7:28, 29—Yesu anati anatumiwa monga woimilako Mulungu, kuonetsa kuti anali wogonjela kwa Yehova
Yoh. 8:29—Yesu anauza omvela ake kuti nthawi zonse anali kucita zinthu zokondweletsa Yehova (w11 3/15 peji 11 pala. 19)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yoh. 7:8-10—Kodi Yesu anawanamiza acibale ake osakhulupilila? (w07 2/1 peji 6 pala. 4)
Yoh. 8:58 nwt-E—N’cifukwa ciani kothela kwa vesiyi kuli mau akuti “nakhala nilipo” m’malo mwa mau akuti “nilipo”? Nanga n’cifukwa ciani zimenezi n’zofunika? (“nakhala nilipo,” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 8:31-47
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndipo itanilani munthuyo ku misonkhano.
Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba na kugaŵila cofalitsa cophunzitsila Baibo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) lv mapeji 9-10 mapa. 10-11
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Onetsani Khalidwe la Kudzicepetsa Monga Khristu”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani mavidiyo onse payokha-payokha.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 36
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 119 na Pemphelo