LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsa. 5
  • November 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 November tsa. 5

November 18-24

CHIVUMBULUTSO 1-3

  • Nyimbo 15 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ndikudziŵa Nchito Zako”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Chivumbulutso.]

    • Chiv. 1:20—Yesu amadziŵa ciliconse cokhudza akulu mu mpingo (w12 10/15 14 ¶8)

    • Chiv. 2:1, 2—Yesu adziŵa zimene zikucitika mu mpingo uliwonse (w12 4/15 29 ¶11; w01 1/15 20-21 ¶20)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Chiv. 1:7—Kodi diso lililonse lidzamuona bwanji Yesu pamene “akubwela ndi mitambo”? Nanga zimenezi zidzacitika liti? (kr 226 ¶8, 10)

    • Chiv. 2:7—Kodi kudya za “mumtengo wa moyo . . .m’paradaiso wa Mulungu” kumatanthauza ciani? (w09 1/15 31 ¶1)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 1:1-11 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno, chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 4

  • “Yehova Adziŵa Zimene Tifunikila”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Lipoti la 2017 la Komiti Yoyang’anila Nchito Yophunzitsa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 91

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 151 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani