LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 January tsa. 2
  • January 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 January tsa. 2

January 6-12

GENESIS 1-2

  • Nyimbo 11 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Analenga Zamoyo pa Dziko Lapansi”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Genesis.]

    • Gen. 1:3, 4, 6, 9, 11—Masiku a kulenga, tsiku loyamba mpaka lacitatu (it-1 527-528)

    • Gen. 1:14, 20, 24, 27—Masiku a kulenga, tsiku lacinayi mpaka la 6 (it-1 528 ¶5-8)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 1:1—Kodi Baibo imakamba kuti dziko lapansi lakhalako kwa nthawi yaitali bwanji? (w15 6/1 5)

    • Gen. 1:26—Kodi Yesu nayenso anali Mlengi? (it-2 52)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 1:1-19 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumveketsa Phindu ya Nkhani, ndiyeno kambilanani phunzilo 13, mu bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w08 2/1 5—Mutu: Timakhala na Mtendele wa mu Mtima Tikadziŵa kuti Tinacita Kulengedwa (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 73

  • “Kodi Mungafotokoze Cikhulupililo Canu?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Dokota Woona za Mafupa Afotokoza Cikhulupililo Cake komanso yakuti Katswili wa za Nyama Afotokoza Cikhulupililo Cake.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 98

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 18 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani