LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 6
  • January 24-30

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 24-30
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 6

January 24-30

RUTE 1-2

  • Nyimbo 108 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitilizani Kuonetsa Cikondi Cosasintha”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Rute 1:20, 21—N’cifukwa ciani Naomi ananena kuti Yehova ndiye anacititsa moyo wake kukhala woŵaŵa? (w05 3/1 27 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Rute 1:1-17 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)

  • Nkhani: (Mph. 5) ia 43-44 ¶5-9—Mutu: Kodi Tikati Banja N’ciani? (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 54

  • “Khalani Otsimikiza za Cikondi Cosasintha ca Yehova”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Lipoti ya 2019 ya Komiti ya Ogwilizanitsa

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 74

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 16 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani