LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 10
  • February 7-13

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 7-13
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 10

February 7-13

1 SAMUELI 1-2

  • Nyimbo 44 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mukhuthulileni za Mumtima Mwanu Yehova M’pemphelo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 2:10—N’cifukwa ciani Hana anapemphela kuti Yehova “apeleke mphamvu kwa mfumu yake” pamene mu Isiraeli munalibe mfumu? (w05 3/15 21 ¶5)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 1:1-18 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kukambilana mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 20)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 03 mfundo 5 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 133

  • “Acinyamata—Auzeni za Mumtima Mwanu Makolo Anu”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Umoyo Wanga Nili Wacicepele—Kodi Ningakambe Nawo Bwanji Makolo Anga?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 76

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 1 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani