LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 3
  • March 14-20

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 14-20
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 3

March 14-20

1 SAMUELI 14-15

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kumvela Kumaposa Nsembe”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 15:24—Kodi pali cenjezo lotani pa cifundo cosayenela cimene Sauli anaonetsa? (it-1 493)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 15:1-16 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Yesu—Mat. 20:28. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani kuti muziphunzila naye Baibo. Kenako, chulani na kukambilanako za mu vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 61

  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso Kudzayamba pa Ciŵelu, pa March 19: (Mph. 10) Kukambilana. Mwacidule, kambilanani zimene zili m’kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso. Fotokozani makonzedwe a pampingo panu okhudza nkhani yapadela na Cikumbutso, komanso a mofolela magawo. Tambitsani na kukambilana vidiyo ya ulaliki wacitsanzo.

  • Khala Bwenzi la Yehova—Mvela Yehova: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 81

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 125 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani