LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 4
  • March 21-27

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 21-27
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 4

March 21-27

1 SAMUELI 16-17

  • Nyimbo 7 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 16:14, na mawu a m’munsi.—Kodi mawu akuti Sauli analandila “mzimu woipa wocokela kwa Yehova” atanthauza ciani? (it-2 871-872)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 16:1-13 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 2) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 11)

  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 3) Itanilani mnzanu wa kunchito, wa kusukulu, kapena wacibale amene munamulalikilapo kale. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso, amenenso anaonetsa cidwi. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso, amenenso anaonetsa cidwi. M’fotokozeleni za webusaiti yathu munthuyo. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 150

  • “Njila Zitatu Zoonetsela Kuti Timadalila Yehova”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Palibe Cifukwa Coopela Cizunzo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 82

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 47 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani