LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 8
  • May 30–June 5

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 30–June 5
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 8

May 30–June 5

2 SAMUELI 7-8

  • Nyimbo 22 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Anacita Pangano na Davide”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 8:2—Kodi ni ulosi uti umene unakwanilitsidwa Davide atagonjetsa Amowabu? (it-2 206 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 7:1-17 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo, ndipo gwilizanitsani makambilanawo na nkhani imene yangocitika kumene. Ndiyeno gaŵilani magazini yofotokoza nkhani imene mwininyumbayo wayambitsa. (th phunzilo 13)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo, ndipo gwilizanitsani makambilanowo na nkhani imene yangocitika kumene. Fotokozani za pulogilamu yathu yaulele yophunzitsa Baibo, ndiyeno gaŵilani munthuyo kakhadi koloŵela pa webusaiti yathu ya jw.org. (th phunzilo 18)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 04 cidule cake, mafunso obweleza, komanso zocita (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 91

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • “Seŵenzetsani Nkhani Zongocitika Kumene mu Ulaliki”: (Mph. 5) Kukambilana.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 06

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo Yatsopano ya pa Msonkhano Wacigawo wa 2022 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani