LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 9
  • June 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 9

June 6-12

2 SAMUELI 9-10

  • Nyimbo 124 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Davide Anaonetsa Cikondi Cosasintha”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 10:4, 5​—N’cifukwa ciyani zimene anacita Hanuni kunali kuwanyoza amuna aciisiraeli? (it-1 266)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 9:1-13 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, mugaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kukambilana naye mwacidule mbali yakuti, “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule Kwambili na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 17)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 05 mfundo 4 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 116

  • Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili—N’cokoma Mtima: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Kenako, funsani omvetsela mafunso awa: Kodi Davide anam’komela mtima motani Mefiboseti? Kodi tingawaonetse bwanji ena kukoma mtima komanso cikondi cosasintha?

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 07

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 1 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani