LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 2
  • July 4-10

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 4-10
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 2

July 4-10

2 SAMUELI 18-19

  • Nyimbo 138 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Barizilai Ni Citsanzo ca Kudzicepetsa”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 19:24-30​—Kodi citsanzo ca Mefiboseti cingatilimbikitse bwanji? (w20.04 30 ¶19)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 19:31-43 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Colinga ca Mulungu—Gen. 1:28. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile (azikidwe) pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba kukambilana, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki.a Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)

  • Nkhani: (Mph. 5) w21.08 23-25 ¶15-19—Mutu: Mungadziikile Zolinga Zotani Ngati Mikhalidwe Siikulolani Kucita Zambili? (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 81

  • “Dziikileni Zolinga za Caka ca Utumiki Catsopano—Kucita Upainiya”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Khalani Olimba Mtima . . . Inu Apainiya.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 11

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 97 na Pemphelo

a Onani nkhani imene ili pa tsamba 16.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani