LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 6
  • July 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 6

July 18-24

2 SAMUELI 22

  • Nyimbo 4 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzidalila Thandizo la Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 22:36—Kodi kudzicepetsa kwa Yehova kunamukweza bwanji Davide? (w12 11/15 17 ¶7)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 22:33-51 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndipo m’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuchulako za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 3)

  • Nkhani: (Mph. 5) w06 8/15 21 ¶7-8—Mutu: Kodi Satana Ndiye Amacititsa Mavuto Onse Amene Timakumana Nawo? (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 12

  • Kondwelani na Nchito za Yehova za Cipulumutso: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo imeneyi. Kenako funsani omvela mafunso awa: Kodi Yehova anathandiza bwanji banja la M’bale Ganeshalingam pa nkhondo ya paciweniweni ku Sri Lanka? Kodi cocitika cimeneci calimbitsa bwanji cikhulupililo canu?

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff mafunso obweleza a cigawo 1

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 60 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani