LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 14
  • August 29–September 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 29–September 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 14

August 29–September 4

1 MAFUMU 8

  • Nyimbo 41 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10.)

    • 1 Maf. 8:27—Kodi mawu a Solomo amenewa satanthauza ciyani? (it-1 1060 ¶4)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 8:31-43 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndipo m’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndipo m’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kuchulako za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 15)

  • Nkhani: (Mph. 5) km 5/10 2—Mutu: Atumiki Acikhristu Amafunika Kupemphela. (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 44

  • “Kodi Mumayesetsa Kuona Mmene Yehova Amayankhila Mapemphelo Anu?”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Yehova ni “Wakumva Pemphelo.”

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 18 mfundo 1-5

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 107 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani