October 3-9
1 MAFUMU 17-18
Nyimbo 32 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mukayika-kayika Mpaka Liti?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Maf. 18:1—N’cifukwa ciyani Yesu anakamba kuti cilala ca m’masiku a Eliya cinatenga “zaka zitatu na miyezi 6”? (Luka 4:25; w08 4/1 19, bokosi)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 18:36-46 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—2 Tim. 3:16, 17. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 12)
Nkhani: (Mph. 5) w14 2/15 14-15—Mutu: Kodi Tingaphunzilepo Ciyani pa Cikhulupililo ca Mkazi Wamasiye? (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 21
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 83 na Pemphelo