LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 10
  • October 10-16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 10-16
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 10

October 10-16

1 MAFUMU 19-20

  • Nyimbo 33 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muziyang’ana kwa Yehova Kuti Mupeze Citonthozo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Maf. 19:19-21—Kodi tiphunzilapo ciyani pa nkhaniyi za kulandila utumiki watsopano? (w97 11/1 31 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 19:1-14 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Baibo—Yobu 26:7. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 18)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 07 mfundo 7, na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 145

  • Musalefuke: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso awa: Ni mfundo za m’Baibo ziti zimene zingatithandize kuti tisalefuke tikakumana na mavuto? Kodi Yehova anam’limbikitsa bwanji Eliya? Nanga Yehova amatitonthoza bwanji na kutisamalila?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 22

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 57 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani