LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 11
  • October 17-23

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 17-23
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 11

October 17-23

1 MAFUMU 21-22

  • Nyimbo 134 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tengelani Citsanzo ca Mmene Yehova Amalamulila”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Maf. 21:27-29—Tidziŵa bwanji kuti zocita za Ahabu sizinaonetse kulapa kwenikweni? (w21.10 3 ¶4-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 22:24-38 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’pempheni kuti muyambe kuphunzila naye Baibo, pogwilitsa nchito kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo m’phunzilo 01. (th phunzilo 6)

  • Nkhani: (Mph. 5) w15 3/15 9-11 ¶10-12—Mutu: Tiphunzilapo Ciyani pa Kukhulupilika kwa Naboti? (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 116

  • “Cikondi N’coleza Mtima Ndiponso N’cokoma Mtima”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso awa: Kodi m’bale Alexandru anaonetsa bwanji kuleza mtima komanso kukoma mtima monga mutu wa banja? N’cifukwa ciyani m’kupita kwa nthawi mkazi wake Dorina anaphunzila coonadi? Nanga tiphunzilapo ciyani pa cocitika cimeneci?

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 23

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 50 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani