LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 14
  • October 31–November 6

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 31–November 6
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 14

October 31–November 6

2 MAFUMU 3-4

  • Nyimbo 151 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nyamulani Mwana Wanu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Maf. 4:38—Kodi “ana a aneneli” ayenela kuti anali ndani? (it-2 697 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Maf. 3:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 17)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 20)

  • Nkhani: (Mph. 5) w13 8/15 28-29—Mutu: Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Elisa ca Kudzicepetsa pa Utumiki Wanu? (th phunzilo 15)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 129

  • “Mpaka Pamene Akufa Adzaukitsidwa”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Munthu Amene Timam’konda Akamwalila.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 25

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 139 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani