LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 6
  • March 27–April 2

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 27–April 2
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 6

March 27–April 2

2 MBIRI 5-7

  • Nyimbo 129 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 6:29, 30—Kodi mawu amenewa a m’pemphelo la Solomo angatilimbikitse bwanji? (w10 12/1 11 ¶7)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 6:28-42 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kuitanila Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mwininyumba akaonetsa cidwi, chulani na kukambilanako vidiyo yakuti Kukumbukila Imfa ya Yesu (koma musaitambitse.) (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Pambuyo pa nkhani ya Cikumbutso, yambitsani makambilano na munthu wacidwi amene wabwela. Ndipo yankhani funso limene wafunsa lokhudza mwambowo. (th phunzilo 17)

  • Nkhani: (Mph. 5) w93 2/1 31—Mutu: Tingacite Ciyani Ngati Sitinakwanitse Kupezeka pa Cikumbutso Cifukwa ca Vuto Linalake Lalikulu? (th phunzilo 18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 36

  • “Uteteze Mtima Wako”: (Mph. 10) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 41 mfundo 5, cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 34 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani