LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 4
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • “Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mungamutumikile Yehova Ngakhale Kuti Makolo anu Sanapeleke Citsanzo Cabwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”

Atawopsezedwa, Yehosafati na anthu a ku Yuda anapemphela kwa Yehova kuti awathandize (2 Mbiri 20:12, 13; w14 12/15 23 ¶8)

Yehova analimbikitsa anthu ake na kuwapatsa malangizo omveka bwino (2 Mbiri 20:17)

Yehova anapulumutsa anthu ake cifukwa anamukhulupilila (2 Mbiri 20:21, 22, 27; w21.11 16 ¶7)

Kagulu ka abale na alongo kasonkhana m’nyumba, pamene apolisi ovala zovala zankhondo komanso onyamula zida akuthyola na kuloŵa m’nyumbamo.

Pamene Gogi adzaukila anthu a Yehova pa cisautso cacikulu, awo amene adzapitiliza kukhulupilila Yehova na kudalila anthu amene iye akuwagwilitsa nchito potsogolela, sadzaopa ciliconse.—2 Mbiri 20:20.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani