LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 7
  • May 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 7

May 22-28

2 MBIRI 25–27

  • Nyimbo 80 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambili Kuposa Pamenepa”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 26:4, 5—Tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca Uziya za kufunika kokhala na m’bale kapena mlongo wokhwima kuuzimu, amene angatithandize kupanga zisankho mwanzelu? (w07 12/15 10 ¶1-2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 25:1-13 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kum’patsa kakhadi kofunsila phunzilo la Baibo. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni za webusaiti yathu na kumugaŵila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 15)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 10 ndime yoyamba, komanso mfundo 1-3 (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 136

  • Khalani Wokonzeka Kudzimana Ciliconse Kuti Mukapeze Moyo Wosatha (Maliko 10:29, 30): (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso aya: Kodi lonjezo la Yesu la pa Maliko 10:29, 30 liyenela kutilimbikitsa kucita ciyani? Kodi Yesu anamvela bwanji pamene abale ake sanamukhulupilile poyamba? Tiyenela kukumbukila ciyani za a m’banja lathu amene si Mboni?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 46

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 51 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani