LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 2
  • July 3-9

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 3-9
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 2

July 3-9

EZARA 4-6

  • Nyimbo 148 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musalowelele Nchito Yomanga Nyumba ya Mulungu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ezara 6:13—N’cifukwa ciyani mawu akuti “Kutsidya la Mtsinje” ni ocititsa cidwi? (w93 6/15 32 ¶3-5)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 4:8-24 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Kuvutika—Yak. 1:13. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kum’siyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kum’patsa kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRITU

  • Nyimbo 7

  • “‘Kuteteza ndi Kukhazikitsa Mwalamulo’ Nchito ya Uthenga Wabwino”: (Mph. 15) Kukambilana komanso kuonelela vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 49 mfundo 6 na cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 130 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani