LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 5
  • July 17-23

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 17-23
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 5

July 17-23

EZARA 9-10

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zotulukapo Zowawa za Kusamvela”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ezara 10:44—N’cifukwa ciyani ana anawacotsa pamodzi na amayi awo? (w06 1/15 20 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 9:1-9 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Seŵenzetsani thilakiti yakuti Kodi Mavuto Adzathadi? poyambitsa makambilanowo. (th phunzilo 13)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano, ndiyeno chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 6)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 ndime yoyamba na mfundo 1-3 (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 150

  • Kumvela Kumatiteteza (2 Ates. 1:8): (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso awa: N’ciyani cidzacitika nkhondo ya Aramagedo isanacitike?

    Kodi timapindula bwanji pali pano cifukwa cokhala omvela?

    Kodi pali kugwilizana kotani pakati pa Aramagedo na kukhala womvela?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 50 mfundo 6-7 na cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 133 na Pempelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani