LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 12
  • August 21-27

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 21-27
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 12

August 21-27

NEHEMIYA 10-11

  • Nyimbo 37 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anadzimana Zinazake Cifukwa Comvela Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Neh. 10:34—N’cifukwa ciyani anthu anafunika kumapeleka nkhuni? (w06 2/1 11 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 10:28-39 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Ndiyeno chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kukambilana mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule Kwambili na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 4)

  • Nkhani: (Mph. 5) w11 2/15 15-16 ¶12-15—Mutu: Nsembe Zimene Mulungu Amakondwela Nazo. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 81

  • “Kodi Zolinga Zanu za Caka Cautumiki Catsopano n’Zotani?”: (Mph. 10) Kukambilana.

  • “Kampeni Yapadela Yolengeza Ufumu wa Mulungu mu September!”: (Mph. 5) Nkhani yokambidwa na woyang’anila utumiki. Limbikitsani ofalitsa kutengako mbali pa kampeniyi, ndipo fotokozani makonzedwe a pa mpingo wanu.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 55 mfundo 1-4

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 92 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani