LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 2
  • September 4-10

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 4-10
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 2

September 4-10

ESITERE 1-2

  • Nyimbo137 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Esitere 2:5—Kodi pali umboni wotani wotsimikizila kuti nkhani ya m’Baibo ya Moredekai ni yoona? (w22.11 31 ¶3-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Esitere 1:​13-22 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Ufumu—Mat 6:​9, 10. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 1)

  • Nkhani: (Mph. 5) w20.11 12-14 ¶3-7—Mutu: Thandizo la Yesu na Angelo. (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 106

  • Zimene Acicepele Anzanu Amakamba—Maonekedwe Anu: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi, kenako funsani omvela mafunso aya: N’cifukwa ciyani kungakhale kovuta kukhala okhutila na maonekedwe athu?

    Kodi mfundo ya pa 1 Petulo 3:​3, 4 ingatithandize bwanji kudziona moyenela?

  • Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya September.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 56 komanso mfundo zakumapeto 6 na 7

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 101 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani