Yophunzila
JANUARY 2020
NKHANI ZOPHUNZILA: MARCH 2–APRIL 5, 2020
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CAKA CA 2020:
“Conco pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzila anga. Muziwabatiza.”—MAT. 28:19.
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PA CIKUTO:
Yesu ataukitsidwa anakumana na atumwi ake na ophunzila ena ku Galileya, ndipo anawalamula kuti “pitani mukaphunzitse anthu . . . kuti akhale ophunzila anga” (Onani nkhani yophunzila 1, ndime 3-4)