Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
KODI MUDZIŴA?
Mulungu Anapereka Mfundo Zokhudza Ukhondo Asayansi Asanazitulukir
Aisiraeli zinthu zinali kuwayendela bwino cifukwa cotsatila malangizo a Mulungu okhudza ukhondo.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > UMBONI WASAYANSI WOSONYEZA KUTI BAIBULO NDI LOLONDOLA.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingakambirane Bwanji ndi Makolo Anga za Malamulo Amene Anakhazikitsa?
Mukamakamba mwaulemu na makolo anu zinthu zingakuyendeleni bwino.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.