Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Luso la Gulugufe Woyera Lotha Kuimitsa Mapiko Ake Ngati V
Kodi ni luso liti la gulugufe woyela limene lathandiza akatswili pokonza mapanelo a sola abwino kwambili?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI > KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Zimene Mungachite Ngati Mumaona Zinthu Mosiyana
Kodi mwamuna na mkazi wake angatani kuti athetse kusamvana popanda kukangana?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > BANJA.