Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
“Ndimachita Zomwe Ndingakwanitse”
Ngakhale kuti ali ndi zaka pafu-pifupi 90, a Irma amalemba makalata ofotokoza mfundo za m’Baibo ndipo anthu ambili amakhudzidwa mtima kwambili akalandila makalatawa.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > KUUZA ENA CHOONADI CHA M’BAIBULO.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Ndingatani Kuti Ndizikonda Masewera Olimbitsa Thupi?
Kuwonjezela pa kukhala ndi thanzi labwino, kodi maseŵela olimbitsa thupi angakuthandizeninso bwanji?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.